Yeremiya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Bwererani inu ana opanduka,” akutero Yehova. “Ine ndakhala mbuye wanu* weniweni. Ine ndidzakutengani, mmodzi kuchokera mumzinda uliwonse, awiri kuchokera mʼbanja lililonse ndipo ndidzakupititsani ku Ziyoni.+
14 “Bwererani inu ana opanduka,” akutero Yehova. “Ine ndakhala mbuye wanu* weniweni. Ine ndidzakutengani, mmodzi kuchokera mumzinda uliwonse, awiri kuchokera mʼbanja lililonse ndipo ndidzakupititsani ku Ziyoni.+