-
Yesaya 61:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Wandituma kuti ndilengeze za chaka cha Yehova chokomera anthu mtima,*
Ndi za tsiku lobwezera la Mulungu wathu,+
Komanso kuti nditonthoze anthu onse amene akulira,+
-