-
Yesaya 3:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Tsoka kwa munthu woipa!
Iye adzakumana ndi mavuto aakulu,
Chifukwa zimene anachitira ena ndi manja ake, nayenso adzamuchitira zomwezo.
-