-
Yeremiya 33:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mzindawu udzakhala ndi dzina limene lidzandisangalatse, udzachititsa kuti nditamandidwe ndiponso kulandira ulemerero pakati pa mitundu yonse yapadziko lapansi, imene idzamve za zinthu zabwino zimene ndinachitira anthu anga.+ Anthu a mitundu inawo adzachita mantha ndipo adzanjenjemera+ chifukwa cha zinthu zonse zabwino komanso mtendere umene ndidzabweretse pa mzindawu.’”+
-