-
Hagai 2:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 ‘Ndigwedeza mitundu yonse ya anthu, ndipo zinthu zamtengo wapatali zochokera ku mitundu yonse ya anthu zidzalowa mʼnyumba imeneyi.+ Ndipo ndidzadzaza nyumbayi ndi ulemerero,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
8 ‘Siliva ndi wanga, golidenso ndi wanga,’ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-