-
Yesaya 42:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Anthu amene amakhala mʼdera lamatanthwe afuule mosangalala.
Anthuwo afuule kuchokera pamwamba pa mapiri.