Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Uzipereka mwana wa nkhosa mmodzi mʼmawa, ndipo mwana wa nkhosa winayo madzulo kuli kachisisira.*+

  • Ekisodo 29:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Mʼmibadwo yanu yonse, muzipereka nsembe yopsereza imeneyi nthawi zonse pakhomo la chihema chokumanako pamaso pa Yehova, kumene ndidzaonekera kwa inu kuti ndilankhule nanu.+

  • Yesaya 56:6, 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ndipo alendo amene abwera kwa Yehova kuti amutumikire,

      Kuti azikonda dzina la Yehova+

      Ndiponso kuti akhale atumiki ake,

      Onse amene amasunga Sabata ndipo salidetsa

      Komanso amene amatsatira pangano langa,

       7 Nawonso ndidzawabweretsa kuphiri langa loyera+

      Ndipo ndidzawachititsa kuti asangalale mʼnyumba yanga yopemphereramo.

      Nsembe zawo zopsereza zathunthu ndi nsembe zawo zina ndidzazilandira paguwa langa lansembe.

      Chifukwa nyumba yanga idzatchedwa nyumba yopemphereramo anthu a mitundu yonse.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena