Hagai 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Ulemerero wa nyumba yatsopanoyi udzakhala waukulu kuposa wa nyumba yoyamba ija,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. ‘Ndipo ndidzakupatsani mtendere pamalo ano,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.”
9 ‘Ulemerero wa nyumba yatsopanoyi udzakhala waukulu kuposa wa nyumba yoyamba ija,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. ‘Ndipo ndidzakupatsani mtendere pamalo ano,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.”