Yesaya 41:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Taona! Onse amene amakupsera mtima adzachita manyazi ndipo adzanyozeka.+ Anthu amene akumenyana nawe adzawonongedwa ndipo adzatha.+
11 Taona! Onse amene amakupsera mtima adzachita manyazi ndipo adzanyozeka.+ Anthu amene akumenyana nawe adzawonongedwa ndipo adzatha.+