Salimo 36:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu ndinu kasupe wa moyo.+Chifukwa cha kuwala kochokera kwa inu, timaona kuwala.+ Yesaya 60:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 “Imirira mkazi iwe!+ Onetsa kuwala kwako, chifukwa kuwala kwako kwafika. Ulemerero wa Yehova wakuunikira.+ Chivumbulutso 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mzindawo sunafunikirenso kuwala kwa dzuwa kapena kwa mwezi, chifukwa kuwala kwa ulemerero wa Mulungu kunkaunikira mzindawo+ ndipo Mwanawankhosa ndi amene anali nyale yake.+ Chivumbulutso 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso, usiku sudzakhalakonso+ ndipo sadzafunikiranso kuwala kwa nyale kapena kwa dzuwa, chifukwa Yehova* Mulungu adzawaunikira.+ Ndipo iwo adzalamulira monga mafumu mpaka kalekale.+
60 “Imirira mkazi iwe!+ Onetsa kuwala kwako, chifukwa kuwala kwako kwafika. Ulemerero wa Yehova wakuunikira.+
23 Mzindawo sunafunikirenso kuwala kwa dzuwa kapena kwa mwezi, chifukwa kuwala kwa ulemerero wa Mulungu kunkaunikira mzindawo+ ndipo Mwanawankhosa ndi amene anali nyale yake.+
5 Komanso, usiku sudzakhalakonso+ ndipo sadzafunikiranso kuwala kwa nyale kapena kwa dzuwa, chifukwa Yehova* Mulungu adzawaunikira.+ Ndipo iwo adzalamulira monga mafumu mpaka kalekale.+