Yesaya 65:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Atumiki anga adzadya, koma inu mudzakhala ndi njala.+ Atumiki anga adzamwa,+ koma inu mudzakhala ndi ludzu. Atumiki anga adzasangalala,+ koma inu mudzachita manyazi.+
13 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Atumiki anga adzadya, koma inu mudzakhala ndi njala.+ Atumiki anga adzamwa,+ koma inu mudzakhala ndi ludzu. Atumiki anga adzasangalala,+ koma inu mudzachita manyazi.+