Yesaya 52:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu+ iwe Ziyoni.+ Vala zovala zako zokongola+ iwe Yerusalemu, mzinda woyera. Chifukwa munthu wosadulidwa ndi wodetsedwa sadzabweranso mwa iwe.+ Chivumbulutso 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinaonanso mzinda woyera, Yerusalemu Watsopano, ukutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu+ ndipo unali utakonzedwa ngati mkwatibwi amene wavala zokongola kuti akalandire mwamuna wake.+
52 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu+ iwe Ziyoni.+ Vala zovala zako zokongola+ iwe Yerusalemu, mzinda woyera. Chifukwa munthu wosadulidwa ndi wodetsedwa sadzabweranso mwa iwe.+
2 Ndinaonanso mzinda woyera, Yerusalemu Watsopano, ukutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu+ ndipo unali utakonzedwa ngati mkwatibwi amene wavala zokongola kuti akalandire mwamuna wake.+