Ekisodo 28:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Uwombe mkanjo wamandalasi ndi ulusi wabwino kwambiri. Upangenso nduwira ya nsalu yabwino kwambiri ndiponso uluke lamba wa mkanjo.+ Ekisodo 28:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Uveke Aroni mʼbale wako pamodzi ndi ana ake zinthu zimenezi. Ukatero uwadzoze,+ uwayeretse nʼkuwaika*+ kuti atumikire monga ansembe anga.
39 Uwombe mkanjo wamandalasi ndi ulusi wabwino kwambiri. Upangenso nduwira ya nsalu yabwino kwambiri ndiponso uluke lamba wa mkanjo.+
41 Uveke Aroni mʼbale wako pamodzi ndi ana ake zinthu zimenezi. Ukatero uwadzoze,+ uwayeretse nʼkuwaika*+ kuti atumikire monga ansembe anga.