Salimo 102:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndithudi inu mudzanyamuka nʼkusonyeza Ziyoni chifundo,+Chifukwa imeneyi ndi nthawi yoti mumusonyeze kukoma mtima kwanu.+Nthawi yoikidwiratu yakwana.+ Zekariya 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova adzatenga Yuda kukhala gawo lake mʼdziko loyera, ndipo adzasankhanso Yerusalemu.+
13 Ndithudi inu mudzanyamuka nʼkusonyeza Ziyoni chifundo,+Chifukwa imeneyi ndi nthawi yoti mumusonyeze kukoma mtima kwanu.+Nthawi yoikidwiratu yakwana.+