Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoweli 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yambani kumweta ndi chikwakwa, chifukwa zokolola zacha.

      Bwerani nʼkuyamba kuponda chifukwa moponderamo mphesa mwadzaza.+

      Malo ogweramo vinyo asefukira, chifukwa zoipa zawo zachuluka kwambiri.

  • Chivumbulutso 14:19, 20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mngeloyo anatsitsira chikwakwa chake padziko lapansi mwamphamvu nʼkumweta mpesa wapadziko lapansi. Kenako anauponya mʼchoponderamo mphesa chachikulu cha mkwiyo wa Mulungu.+ 20 Anapondaponda mopondera mphesamo kunja kwa mzinda ndipo magazi anatuluka mʼchoponderamo mphesacho mpaka kufika mʼzibwano za mahatchi, nʼkuyenderera mtunda wa masitadiya 1,600.*

  • Chivumbulutso 19:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mʼkamwa mwake munkatuluka lupanga lalitali+ lakuthwa, loti aphere mitundu ya anthu ndipo adzawakusa ndi ndodo yachitsulo.+ Komanso iye ankapondaponda muchopondera mphesa cha mkwiyo waukulu wa Mulungu Wamphamvuyonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena