Yeremiya 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndidzamenyana nanu+ ndi mkono wotambasula ndiponso dzanja lamphamvu. Ndidzachita zimenezi nditakwiya, nditapsa mtima komanso ndili ndi ukali waukulu.+
5 Ine ndidzamenyana nanu+ ndi mkono wotambasula ndiponso dzanja lamphamvu. Ndidzachita zimenezi nditakwiya, nditapsa mtima komanso ndili ndi ukali waukulu.+