Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 11:16, 17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Yehova anayankha Mose kuti: “Undisonkhanitsire akulu 70 pakati pa akulu a Isiraeli, amene umawaona* kuti ndi akulu komanso oyangʼanira pakati pa anthuwo.+ Upite nawo kuchihema chokumanako, ndipo akaime kumeneko limodzi ndi iwe. 17 Ine ndibwera kumeneko+ kudzalankhula nawe+ ndipo ndidzatenga gawo lina la mzimu+ umene uli pa iwe nʼkuuika pa anthuwo. Pamenepo iwo adzatha kukuthandiza kusenza udindo woyangʼanira anthuwo, kuti usausenze wekha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena