Yesaya 41:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Usachite mantha, nyongolotsi* iwe Yakobo,+Inu amuna a mu Isiraeli, ineyo ndikuthandizani,” akutero Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli.
14 “Usachite mantha, nyongolotsi* iwe Yakobo,+Inu amuna a mu Isiraeli, ineyo ndikuthandizani,” akutero Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli.