2 Mbiri 36:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inatentha nyumba ya Mulungu woona,+ kugwetsa mpanda wa Yerusalemu,+ kutentha nyumba zonse zokhala ndi mipanda yolimba kwambiri ndiponso zinthu zonse zamtengo wapatali.+ Yesaya 64:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nyumba yathu yoyera* ndiponso yaulemerero,*Imene makolo athu ankakutamandiranimo,Yawotchedwa ndi moto,+Ndipo zinthu zathu zonse zimene tinkaziona kuti ndi zamtengo wapatali zasanduka mabwinja Maliro 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mdani wamulanda zinthu zake zonse zamtengo wapatali.+ Yerusalemu waona anthu a mitundu ina akulowa mʼmalo ake opatulika,+Mitundu imene munalamula kuti isamalowe mumpingo wanu.
19 Inatentha nyumba ya Mulungu woona,+ kugwetsa mpanda wa Yerusalemu,+ kutentha nyumba zonse zokhala ndi mipanda yolimba kwambiri ndiponso zinthu zonse zamtengo wapatali.+
11 Nyumba yathu yoyera* ndiponso yaulemerero,*Imene makolo athu ankakutamandiranimo,Yawotchedwa ndi moto,+Ndipo zinthu zathu zonse zimene tinkaziona kuti ndi zamtengo wapatali zasanduka mabwinja
10 Mdani wamulanda zinthu zake zonse zamtengo wapatali.+ Yerusalemu waona anthu a mitundu ina akulowa mʼmalo ake opatulika,+Mitundu imene munalamula kuti isamalowe mumpingo wanu.