Yeremiya 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma anthu awa ali ndi mtima wosamvera komanso wopanduka.Achoka panjira yanga ndipo akuyenda mʼnjira yawo.+
23 Koma anthu awa ali ndi mtima wosamvera komanso wopanduka.Achoka panjira yanga ndipo akuyenda mʼnjira yawo.+