Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 7:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kenako Yoswa ndi Aisiraeli onse anatenga Akani+ mwana wa Zera, limodzi ndi siliva uja, chovala chamtengo wapatali chija, mtanda wa golide uja,+ komanso ana ake aamuna ndi aakazi, ngʼombe zake, abulu, nkhosa, ndiponso hema wake, ndi chilichonse chomwe chinali chake, nʼkupita nawo kuchigwa cha Akori.+

  • Hoseya 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kuyambira nthawi imeneyo kupita mʼtsogolo ndidzamubwezera minda yake ya mpesa.+

      Ndidzamupatsanso chigwa cha Akori+ kuti chikhale ngati khomo lachiyembekezo.

      Kumeneko adzayankha ngati mmene ankayankhira ali mtsikana,

      Ngatinso pa tsiku limene anatuluka mʼdziko la Iguputo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena