24 Kuwonjezera pamenepo, Ahazi anasonkhanitsa ziwiya zamʼnyumba ya Mulungu woona+ nʼkuziphwanyaphwanya. Komanso anatseka zitseko za nyumba ya Yehova.+ Kenako anadzimangira maguwa ansembe mʼmakona onse a mu Yerusalemu.
25 chifukwa chakuti andisiya+ nʼkumakapereka nsembe zautsi kwa milungu ina kuti andikwiyitse+ ndi ntchito zonse za manja awo, ndibweretsa mkwiyo wanga pamalo ano ndipo suzimitsidwa.’”+