Yesaya 62:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Mitundu ya anthu idzaona kulungama kwako mkazi iwe,+Ndipo mafumu onse adzaona ulemerero wako.+ Iwe udzapatsidwa dzina latsopano+Limene Yehova adzasankhe.* Yeremiya 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mʼmasiku amenewo Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Yerusalemu adzakhala mwamtendere.+ Yerusalemu azidzatchulidwa kuti, Yehova Ndi Chilungamo Chathu.’”+
2 “Mitundu ya anthu idzaona kulungama kwako mkazi iwe,+Ndipo mafumu onse adzaona ulemerero wako.+ Iwe udzapatsidwa dzina latsopano+Limene Yehova adzasankhe.*
16 Mʼmasiku amenewo Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Yerusalemu adzakhala mwamtendere.+ Yerusalemu azidzatchulidwa kuti, Yehova Ndi Chilungamo Chathu.’”+