Yesaya 51:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu owomboledwa a Yehova adzabwerera.+ Adzabwera ku Ziyoni akufuula mosangalala,+Ndipo pamutu pawo padzakhala chisangalalo mpaka kalekale.+ Iwo adzapeza chisangalalo ndi chimwemwe,Ndipo chisoni komanso kulira zidzachoka.+
11 Anthu owomboledwa a Yehova adzabwerera.+ Adzabwera ku Ziyoni akufuula mosangalala,+Ndipo pamutu pawo padzakhala chisangalalo mpaka kalekale.+ Iwo adzapeza chisangalalo ndi chimwemwe,Ndipo chisoni komanso kulira zidzachoka.+