-
Yesaya 62:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Koma dzina lako lidzakhala Ndimakondwera Naye,+
Ndipo dziko lako lidzatchedwa Mkazi Wokwatiwa.
Chifukwa Yehova adzasangalala nawe,
Ndipo dziko lako lidzakhala ngati mkazi wokwatiwa.
-