Yohane 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Siyani kuweruza potengera maonekedwe akunja, koma muziweruza ndi chiweruzo cholungama.”+ Yohane 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ndikati ndiweruze, chiweruzo changa chimakhala cholungama, chifukwa sindiweruza ndekha koma ine limodzi ndi Atate amene anandituma timaweruzira limodzi.+
16 Koma ndikati ndiweruze, chiweruzo changa chimakhala cholungama, chifukwa sindiweruza ndekha koma ine limodzi ndi Atate amene anandituma timaweruzira limodzi.+