2 Atesalonika 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako, wosamvera malamuloyo adzaonekera poyera. Ambuye Yesu adzathetsa wosamvera malamuloyu ndi mzimu wamʼkamwa mwake+ ndipo adzamuwonongeratu pa nthawi imene kukhalapo kwa Yesuyo kudzaonekere.+
8 Kenako, wosamvera malamuloyo adzaonekera poyera. Ambuye Yesu adzathetsa wosamvera malamuloyu ndi mzimu wamʼkamwa mwake+ ndipo adzamuwonongeratu pa nthawi imene kukhalapo kwa Yesuyo kudzaonekere.+