Yeremiya 44:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno amuna onse amene ankadziwa kuti akazi awo ankapereka nsembe kwa milungu ina, akazi onse amene anaimirira nʼkupanga gulu lalikulu komanso anthu onse amene ankakhala ku Iguputo+ mʼdera la Patirosi,+ anayankha Yeremiya kuti:
15 Ndiyeno amuna onse amene ankadziwa kuti akazi awo ankapereka nsembe kwa milungu ina, akazi onse amene anaimirira nʼkupanga gulu lalikulu komanso anthu onse amene ankakhala ku Iguputo+ mʼdera la Patirosi,+ anayankha Yeremiya kuti: