19 Uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine nditenga ndodo ya Yosefe ndi mafuko a Isiraeli amene ali naye. Ndodo imeneyi ili mʼdzanja la Efuraimu. Ndidzaiphatikiza ndi ndodo ya Yuda ndipo idzakhala ndodo imodzi.+ Iwo adzakhala ndodo imodzi mʼdzanja langa.”’