Salimo 118:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ya ndi malo anga obisalapo komanso mphamvu yanga,Iye wakhala chipulumutso changa.+ Hoseya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ndidzachitira chifundo anthu a mʼnyumba ya Yuda+ ndipo Ine Yehova Mulungu wawo ndidzawapulumutsa.+ Sindidzawapulumutsa ndi nkhondo, uta, lupanga, mahatchi* kapenanso amuna okwera pamahatchi.”+
7 Koma ndidzachitira chifundo anthu a mʼnyumba ya Yuda+ ndipo Ine Yehova Mulungu wawo ndidzawapulumutsa.+ Sindidzawapulumutsa ndi nkhondo, uta, lupanga, mahatchi* kapenanso amuna okwera pamahatchi.”+