Zekariya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Fuulanso kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Mizinda yanga idzasefukiranso ndi zinthu zabwino. Yehova adzalimbikitsanso Ziyoni+ ndipo adzasankhanso Yerusalemu.”’”+
17 Fuulanso kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Mizinda yanga idzasefukiranso ndi zinthu zabwino. Yehova adzalimbikitsanso Ziyoni+ ndipo adzasankhanso Yerusalemu.”’”+