Mika 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu mapiri akuluakulu, imvani mlandu umene Yehova ali nawo pa anthu ake.Mvetserani inu maziko a dziko lapansi,+Chifukwa Yehova ali ndi mlandu ndi anthu ake.Iye azenga mlandu Aisiraeli, kuti:+ Yakobo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yandikirani Mulungu ndipo iyenso adzakuyandikirani.+ Yeretsani manja anu ochimwa inu,+ ndipo yeretsani mitima yanu+ okayikakayika inu.
2 Inu mapiri akuluakulu, imvani mlandu umene Yehova ali nawo pa anthu ake.Mvetserani inu maziko a dziko lapansi,+Chifukwa Yehova ali ndi mlandu ndi anthu ake.Iye azenga mlandu Aisiraeli, kuti:+
8 Yandikirani Mulungu ndipo iyenso adzakuyandikirani.+ Yeretsani manja anu ochimwa inu,+ ndipo yeretsani mitima yanu+ okayikakayika inu.