Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Hoseya 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ine ndidzawombola anthu anga ku mphamvu za Manda.*

      Ndidzawapulumutsa ku imfa.+

      Iwe Imfa amene umabweretsa ululu woopsa, kodi mphamvu yako ili kuti?+

      Iwe Manda, kodi mphamvu yako yowononga ili kuti?+

      Koma Efuraimu sindimumvera chisoni.

  • 1 Akorinto 15:54
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 Koma matupi oti akhoza kuwonongekawa akadzakhala oti sangawonongeke komanso matupi oti angafewa akadzasintha nʼkukhala oti sangafe, zimene Malemba amanena zidzakwaniritsidwa, zakuti: “Imfa yamezedwa* kwamuyaya.”+

  • 2 Timoteyo 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma tsopano izi zatsimikizirika chifukwa cha kuonekera kwa Mpulumutsi wathu Khristu Yesu,+ amene wathetsa mphamvu za imfa.+ Komanso pogwiritsa ntchito uthenga wabwino,+ watidziwitsa mmene tingapezere moyo+ wosawonongeka.+

  • Chivumbulutso 20:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndipo imfa ndi Manda* zinaponyedwa mʼnyanja yamoto.+ Nyanja yamoto+ imeneyi ikuimira imfa yachiwiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena