-
Zefaniya 2:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo,
Mowabu adzakhala ngati Sodomu,+
Ndipo Amoni adzakhala ngati Gomora,+
Malo okhala ndi zomera zoyabwa, dothi lamchere ndiponso malo abwinja mpaka kalekale.+
Anthu anga amene adzatsale adzatenga zinthu za anthu amenewa,
Ndipo anthu amtundu wanga amene adzatsale, adzawalanda anthuwa zinthu zawo.
-