Yeremiya 48:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Tamva za kunyada kwa Mowabu. Iye ndi wodzikuza kwambiri.Tamva za kudzitukumula kwake, kunyada kwake, kudzikweza kwake ndi kudzikuza kwa mtima wake.”+ Yakobo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komabe, kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu amapereka kumaposa khalidwe limeneli. Nʼchifukwa chake lemba limati: “Mulungu amatsutsa odzikuza,+ koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.”+
29 “Tamva za kunyada kwa Mowabu. Iye ndi wodzikuza kwambiri.Tamva za kudzitukumula kwake, kunyada kwake, kudzikweza kwake ndi kudzikuza kwa mtima wake.”+
6 Komabe, kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu amapereka kumaposa khalidwe limeneli. Nʼchifukwa chake lemba limati: “Mulungu amatsutsa odzikuza,+ koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.”+