Yesaya 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsoka kwa anthu amene amapita ku Iguputo kukapempha thandizo,+Amene amadalira mahatchi,+Amene amadalira magaleta ankhondo chifukwa chakuti ndi ambiri,Komanso mahatchi ankhondo* chifukwa chakuti ndi amphamvu kwambiri. Koma sayangʼana kwa Woyera wa Isiraeli,Ndipo safunafuna Yehova. Ezekieli 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho anthu onse amene akukhala ku Iguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova,Chifukwa sanalinso ngati ndodo yothandiza nyumba ya Isiraeli poyenda, koma anali ngati tsekera.*+
31 Tsoka kwa anthu amene amapita ku Iguputo kukapempha thandizo,+Amene amadalira mahatchi,+Amene amadalira magaleta ankhondo chifukwa chakuti ndi ambiri,Komanso mahatchi ankhondo* chifukwa chakuti ndi amphamvu kwambiri. Koma sayangʼana kwa Woyera wa Isiraeli,Ndipo safunafuna Yehova.
6 Choncho anthu onse amene akukhala ku Iguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova,Chifukwa sanalinso ngati ndodo yothandiza nyumba ya Isiraeli poyenda, koma anali ngati tsekera.*+