Yesaya 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akalonga a ku Zowani+ ndi opusa. Alangizi anzeru kwambiri a Farao, amapereka malangizo osathandiza.+ Koma zoona mungamuuze Farao kuti: “Ine ndine mbadwa ya anthu anzeru,Ndine mbadwa ya mafumu akale”? Ezekieli 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mzinda wa Patirosi+ ndidzausandutsa bwinja. Mzinda wa Zowani ndidzauwotcha ndi moto ndipo ndidzaweruza mzinda wa No.*+
11 Akalonga a ku Zowani+ ndi opusa. Alangizi anzeru kwambiri a Farao, amapereka malangizo osathandiza.+ Koma zoona mungamuuze Farao kuti: “Ine ndine mbadwa ya anthu anzeru,Ndine mbadwa ya mafumu akale”?
14 Mzinda wa Patirosi+ ndidzausandutsa bwinja. Mzinda wa Zowani ndidzauwotcha ndi moto ndipo ndidzaweruza mzinda wa No.*+