Yesaya 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova anandiuza kuti: “Tenga cholembapo chachikulu+ ndipo ulembepo ndi cholembera wamba* kuti, ‘Maheri-salala-hasi-bazi.’* Yeremiya 36:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tenga mpukutu ndipo ulembemo mawu onse amene ndakuuza okhudza chilango chimene ndidzapereke kwa Isiraeli, Yuda+ ndi mitundu yonse ya anthu.+ Ulembe mawu onse amene ndakuuza kuchokera nthawi imene ndinalankhula nawe mʼmasiku a Yosiya mpaka lero.+
8 Yehova anandiuza kuti: “Tenga cholembapo chachikulu+ ndipo ulembepo ndi cholembera wamba* kuti, ‘Maheri-salala-hasi-bazi.’*
2 “Tenga mpukutu ndipo ulembemo mawu onse amene ndakuuza okhudza chilango chimene ndidzapereke kwa Isiraeli, Yuda+ ndi mitundu yonse ya anthu.+ Ulembe mawu onse amene ndakuuza kuchokera nthawi imene ndinalankhula nawe mʼmasiku a Yosiya mpaka lero.+