Amosi 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma usapitirize kunenera ku Beteli kuno,+ chifukwa ndi malo opatulika a mfumu+ ndiponso nyumba ya ufumuwu.” Amosi 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano imva zimene Yehova wanena, ‘Ukunena kuti: “Usanenere zinthu zoipa zokhudza Isiraeli,+ ndipo usanene mawu alionse+ oipa okhudza nyumba ya Isaki.”
13 Koma usapitirize kunenera ku Beteli kuno,+ chifukwa ndi malo opatulika a mfumu+ ndiponso nyumba ya ufumuwu.”
16 Tsopano imva zimene Yehova wanena, ‘Ukunena kuti: “Usanenere zinthu zoipa zokhudza Isiraeli,+ ndipo usanene mawu alionse+ oipa okhudza nyumba ya Isaki.”