Levitiko 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndidzaika mantha mʼmitima ya anthu amene adzapulumuke+ omwe akukhala mʼdziko la adani awo, moti adzathawa phokoso la tsamba louluka. Iwo adzathawa ngati munthu amene akuthawa lupanga, moti adzagwa popanda wowathamangitsa.+ Deuteronomo 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kodi munthu mmodzi angathamangitse bwanji anthu 1,000,Kapena anthu awiri angathamangitse bwanji anthu 10,000?+ Nʼzosatheka, pokhapokha Thanthwe lawo litawagulitsa,+Komanso ngati Yehova atawapereka.
36 Ndidzaika mantha mʼmitima ya anthu amene adzapulumuke+ omwe akukhala mʼdziko la adani awo, moti adzathawa phokoso la tsamba louluka. Iwo adzathawa ngati munthu amene akuthawa lupanga, moti adzagwa popanda wowathamangitsa.+
30 Kodi munthu mmodzi angathamangitse bwanji anthu 1,000,Kapena anthu awiri angathamangitse bwanji anthu 10,000?+ Nʼzosatheka, pokhapokha Thanthwe lawo litawagulitsa,+Komanso ngati Yehova atawapereka.