Salimo 99:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi mfumu yamphamvu imene imakonda chilungamo.+ Nthawi zonse mumaonetsetsa kuti chilungamo chachitika. Mwabweretsa chiweruzo cholungama komanso chilungamo+ pakati pa ana a Yakobo. Yeremiya 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Inu Yehova, ndilangizeni pondipatsa chiweruzo,Koma osati mutakwiya+ chifukwa mungandiwononge.+
4 Iye ndi mfumu yamphamvu imene imakonda chilungamo.+ Nthawi zonse mumaonetsetsa kuti chilungamo chachitika. Mwabweretsa chiweruzo cholungama komanso chilungamo+ pakati pa ana a Yakobo.