-
Yobu 36:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Pajatu Mulungu ali ndi mphamvu zapamwamba.
Kodi pali mphunzitsi winanso wofanana naye?
-
-
Salimo 119:102Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
102 Sindinasiye kutsatira zigamulo zanu,
Chifukwa inu mwandilangiza.
-