Yeremiya 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Ine ndichiritsa anthu amumzindawu nʼkuwapatsa thanzi labwino.+ Ndiwachiritsa nʼkuwapatsa mtendere wambiri ndi choonadi chochuluka.+ Amosi 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ‘Pa tsiku limenelo, ndidzadzutsa nyumba* ya Davide+ imene inagwa,Ndi kukonza malo amene khoma lake linawonongeka.Ndidzaikonza kuti isakhalenso bwinja.Ndipo ndidzaimanga kuti ikhale ngati mmene inalili kale.+
6 ‘Ine ndichiritsa anthu amumzindawu nʼkuwapatsa thanzi labwino.+ Ndiwachiritsa nʼkuwapatsa mtendere wambiri ndi choonadi chochuluka.+
11 ‘Pa tsiku limenelo, ndidzadzutsa nyumba* ya Davide+ imene inagwa,Ndi kukonza malo amene khoma lake linawonongeka.Ndidzaikonza kuti isakhalenso bwinja.Ndipo ndidzaimanga kuti ikhale ngati mmene inalili kale.+