-
Ekisodo 15:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Kenako Miriamu, mneneri wamkazi, yemwe anali mchemwali wake wa Aroni, anatenga maseche mʼmanja mwake ndipo akazi ena onse ankamutsatira akuimba maseche nʼkumavina.
-