Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 5:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Chifukwa pakati pa anthu anga pali anthu oipa.

      Iwo amabisala nʼkumayangʼanitsitsa ngati mmene amachitira wosaka mbalame.

      Amatchera msampha wakupha

      Ndipo amagwira anthu.

  • Mika 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Manja awo amachita zoipa ndipo amazichita mwaukatswiri kwambiri.+

      Kalonga amalamula kuti amupatse mphatso,

      Woweruza amauza anthu kuti amupatse chiphuphu.+

      Munthu wotchuka amauza anthu zimene akulakalaka,+

      Ndipo onsewa amakonzera limodzi chiwembu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena