Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 37:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndidzachita nawo pangano lamtendere+ ndipo pangano limeneli lidzakhalapo mpaka kalekale. Ine ndidzachititsa kuti akhazikike mʼdzikolo ndipo ndidzawachulukitsa+ komanso ndidzaika malo anga opatulika pakati pawo mpaka kalekale.

  • Mika 4:3, 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Mulungu adzaweruza mitundu yambiri ya anthu,+

      Ndipo adzakonza zinthu zolakwika zokhudza anthu ochokera mʼmitundu yamphamvu yakutali.

      Iwo adzasula malupanga awo kuti akhale makasu a pulawo,

      Ndiponso mikondo yawo kuti ikhale zida zosadzira mitengo.+

      Mtundu wa anthu sudzanyamula lupanga kuti umenyane ndi mtundu unzake,

      Ndipo anthuwo sadzaphunziranso nkhondo.+

       4 Aliyense adzakhala pansi pa mtengo wake wa mpesa ndi mtengo wake wa mkuyu,+

      Ndipo sipadzakhala wowaopseza,+

      Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena zimenezi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena