2 Mafumu 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mʼchaka cha 14 cha Mfumu Hezekiya, Senakeribu mfumu ya Asuri+ anabwera kudzaukira mizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri ndipo analanda mizindayo.+ Yesaya 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye wanena kuti: “Eya! Onani Msuri,+Iye ndi ndodo yosonyezera mkwiyo wanga+Ndipo ndigwiritsa ntchito chikwapu chimene chili mʼdzanja lake popereka chilango.
13 Mʼchaka cha 14 cha Mfumu Hezekiya, Senakeribu mfumu ya Asuri+ anabwera kudzaukira mizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri ndipo analanda mizindayo.+
5 Iye wanena kuti: “Eya! Onani Msuri,+Iye ndi ndodo yosonyezera mkwiyo wanga+Ndipo ndigwiritsa ntchito chikwapu chimene chili mʼdzanja lake popereka chilango.