Salimo 123:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mofanana ndi mmene maso a atumiki amayangʼanira dzanja la mbuye wawo,Komanso mmene maso a kapolo wamkazi amayangʼanira dzanja la mbuye wake wamkazi,Maso athu akuyangʼana kwa Yehova Mulungu wathu,+Mpakana atatikomera mtima.+
2 Mofanana ndi mmene maso a atumiki amayangʼanira dzanja la mbuye wawo,Komanso mmene maso a kapolo wamkazi amayangʼanira dzanja la mbuye wake wamkazi,Maso athu akuyangʼana kwa Yehova Mulungu wathu,+Mpakana atatikomera mtima.+