Salimo 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mulungu ndi pothawira pathu komanso mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya mavuto.+ Nahumu 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ndi wabwino+ ndipo ndi malo achitetezo pa nthawi yamavuto.+ Amadziwa* amene amathawira kwa iye kuti apeze chitetezo.+
46 Mulungu ndi pothawira pathu komanso mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya mavuto.+
7 Yehova ndi wabwino+ ndipo ndi malo achitetezo pa nthawi yamavuto.+ Amadziwa* amene amathawira kwa iye kuti apeze chitetezo.+