-
Deuteronomo 28:66, 67Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
66 Moyo wanu udzakhala pangozi yaikulu koopsa, ndipo mudzakhala mwamantha usiku ndi masana, moti simudzakhala wotsimikiza ngati mudzakhalebe ndi moyo. 67 Mʼmawa mudzanena kuti, ‘Zikanakhala bwino akanakhala madzulo!’ ndipo madzulo mudzanena kuti, ‘Zikanakhala bwino ukanakhala mʼmawa!’ chifukwa cha mantha amene adzagwire mtima wanu, ndiponso chifukwa cha zimene maso anu adzaone.
-